Proverbs 31:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mkazi wolemerera angathe kumpeza ndani? Ndi wokwera mtengo kuposa miyala ya yamtengowapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkazi wangwiro ndani angampeze? Pakuti mtengo wake uposa ngale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mkazi wangwiro angathe kumupeza ndani? Ndi wokwera mtengo kuposa miyala yamtengowapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkazi wangwiro ndani angampeze? Pakuti mtengo wace uposa ngale.