Proverbs 31:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wa mwamuna wake umamkhulupirira, ndipo mwamunayo sadzasoŵa phindu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wa mwamuna wake umkhulupirira, sadzasowa phindu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wa mwamuna wake umamukhulupirira ndipo mwamunayo sasowa phindu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wa mwamuna wace umkhulupirira, Sadzasowa phindu.