Proverbs 31:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amadzuka usikusiku nkuyamba kukonzera chakudya anthu a pabanja pake, ndi kuŵagaŵira ntchito adzakazi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aukanso kusanake, napatsa banja lake zakudya, nagawira adzakazi ake ntchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amadzuka kusanache kwenikweni; ndi kuyamba kukonzera a pa banja pake chakudya ndi kuwagawira ntchito atsikana ake antchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aukanso kusanace, Napatsa banja lace zakudya, nagawira adzakazi ace nchito.