Proverbs 31:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchiyani, mwana wanga? Nchiyani, mwana wa m'mimba mwanga? Nchiyani, mwana wanga amene ndidachita kukupempha polonjeza ndi malumbiro?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chiyani mwananga, Chiyani mwana wa mimba yanga? Chiyani mwana wa zowinda zanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchiyani mwana wanga? Nʼchiyani mwana wa mʼmimba mwanga? Nʼchiyani iwe mwana wanga amene ndinachita kupempha ndi malumbiro?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ciani mwananga, Ciani mwana wa mimba yanga? Ciani mwana wa zowinda zanga?