Proverbs 31:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A pabanja pake saŵaopera kuti nkufa nacho chisanu, poti amadziŵa kuti onsewo amavala zovala zofunda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Saopera banja lake chipale chofewa; pakuti banja lake lonse livala mlangali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye saopa kuti banja lake lifa ndi kuzizira pa nyengo yachisanu; pakuti onse amakhala atavala zovala zofunda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Saopera banja lace cipale cofewa; Pakuti banja lace lonse libvala mlangali.