Proverbs 31:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amadzipangira yekha zofunda, ndipo iye amavala zovala zabafuta ndi za mtengo wapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzipangira zimbwi zamawangamawanga; navala bafuta ndi guta wofiirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amadzipangira yekha zoyala pa bedi pake; amavala zovala zabafuta ndi zapepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzipangira zimbwi zamaangamaanga; Nabvala bafuta ndi guta woti biriwiri.