Proverbs 31:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwamuna wake ndi wodziŵika ndithu ku mabwalo, akakhala pakati pa akuluakulu a dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamuna wake adziwika kubwalo, pokhala pakati pa akulu a dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwamuna wake ndi wodziwika pa chipata cha mzinda, ndipo amakhala pakati pa akuluakulu a mʼdzikomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamuna wace adziwika kubwalo, Pokhala pakati pa akuru a dziko.