Proverbs 31:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkazi ameneyu amasoka zovala za nsalu yabafuta, nazigulitsa, amaperekanso mipango kwa anthu amalonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asoka malaya abafuta, nawagulitsa; napereka mipango kwa ogulitsa malonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amasoka nsalu zabafuta nazigulitsa; amaperekanso mipango kwa anthu amalonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asoka maraya abafuta, nawagulitsa; Napereka mipango kwa wogulitsa malonda.