Proverbs 31:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana ake amamnyadira nkumutchula kuti ndi wodala. Mwamuna wake nayenso amamtamanda, amati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anake adzanyamuka, nadzamutcha wodala; mwamuna wake namtama, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana ake amamunyadira ndipo amamutcha kuti wodala; ndipo mwamuna wake, amamuyamikira nʼkumati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anace adzanyamuka, nadzamucha wodala; Mwamuna wace namtama, nati,