Proverbs 31:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inde alipo akazi ambiri olemerera kwabasi, koma kuyerekeza ndi iwe, onsewo nchabe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana akazi ambiri anachita mwangwiro, koma iwe uposa onsewo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pali akazi ambiri amene achita zinthu zopambana koma iwe umawaposa onsewa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana akazi ambiri anacita mwangwiro, Koma iwe uposa onsewo.