Proverbs 31:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphamvu zako usathere pa akazi, usamayenda nawo ameneŵa, amaononga ndi mafumu omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musapereke mphamvu yako kwa akazi, ngakhale kuyenda m'njira yoononga mafumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usapereke mphamvu yako kwa akazi. Usamayenda nawo amenewa popeza amawononga ngakhale mafumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musapereke mphamvu yako kwa akazi, Ngakhale kuyenda m'njira yoononga mafumu.