Proverbs 31:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuwopa kuti angaiŵale malamulo a dziko, ndi kukhotetsa zinthu zoyenerera anthu osauka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti angamwe, naiwale malamulo, naweruze mokhota anthu onse osautsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuopa kuti akamwa adzayiwala malamulo a dziko, nayamba kukhotetsa zinthu zoyenera anthu osauka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti angamwe, naiwale malamulo, Naweruze mokhota anthu onse osautsidwa.