Proverbs 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, umvetsere bwino zanzeru ndikukuuzazi, utchere khutu kwa ine womvetsa bwino zinthu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, mvera nzeru yanga; tcherera makutu ku luntha langa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, mvetsera bwino za nzeru zimene ndikukuwuzazi, tchera khutu ku mawu odziwitsa bwino zinthu ndikukupatsa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, mvera nzeru yanga; Cherera makutu ku luntha langa;