Proverbs 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwinanso alendo adzadyerera chuma chako, phindu la ntchito zako lidzagwa m'manja mwa munthu wachilendo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mphamvu yako isakhutitse alendo, ndi kuti usagwire ntchito m'nyumba ya wachilendo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapenanso alendo angadyerere chuma chako ndi phindu la ntchito yako kulemeretsa anthu ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti mphamvu yako isakhutitse alendo, Ndi kuti usagwire nchito m'nyumba ya wacilendo;