Proverbs 5:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo iwe udzangoti, “Kalanga ine, ndinkadana nkusunga mwambo, mtima wanga unkanyoza chidzudzulo!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti, Bwanji ndinada mwambo, mtima wanga ndi kunyoza chidzudzulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo udzati, “Mayo ine, ndinkadana ndi kusunga mwambo! Mtima wanga unkanyoza chidzudzulo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kuti, Bwanji ndinada mwambo, Mtima wanga ndi kunyoza cidzudzulo;