Proverbs 5:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti uziganiza mochenjera, ndipo pakamwa pako pazilankhula zanzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ukasunge zolingalira, milomo yako ilabadire zomwe udziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti uthe kuchita zinthu mochenjera ndi mwanzeru ndiponso kuti utetezedwe ku mayankhulidwe a mkazi wachilendo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukasunge zolingalira, Milomo yako ilabadire zomwe udziwa.