Proverbs 5:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, ungakopekerenji ndi mkazi wadama, ungamkumbatire bwanji mkazi wosakhala wako?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ukondwerenji, mwananga, ndi mkazi wachiwerewere, ndi kufungatira chifuwa cha mkazi wachilendo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, nʼchifukwa chiyani ukukopeka ndi mkazi wachigololo? Bwanji ukukumbatira mkazi wachilendo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ukondwerenji, mwananga, ndi mkazi waciwerewere, Ndi kufungatira cifuwa ca mkazi wacilendo?