Proverbs 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mkazi wadama ali ndi pakamwa pokoma ngati uchi, mau ake ndi osalala koposa mafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti milomo ya mkazi wachiwerewere ikukha uchi; m'kamwa mwake muti see koposa mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mkazi wachigololo ali ndi mawu okoma ngati uchi. Zoyankhula zake ndi zosalala ngati mafuta,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti milomo ya mkazi waciwerewere ikukha uci; M'kamwa mwace muti see koposa mafuta.