Proverbs 5:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kotsiriza kwake ngwoŵaŵa ngati chivumulo, ngwolasa ngati lupanga lakuthwa konsekonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimaliziro chake nchowawa ngati chivumulo, ndi chakuthwa ngati lupanga lakuthawa konsekonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma kotsirizira kwake ngowawa ngati ndulu; ngakuthwa ngati lupanga lakuthwa konsekonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimariziro cace ncowawa ngati civumulo, Ndi cakuthwa ngati lupanga lakuthwa konse konse.