Proverbs 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwinamwina ulemu wako udzalanditsa kwa ena, zaka zako zaunyamata udzazitaya kwa anthu ankhanza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ungapereke ulemu wako kwa ena, ndi zaka zako kwa ankhanza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuopa kuti ungadzalanditse ulemerero wako kwa anthu ena; ndi zaka zako kwa anthu ankhanza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ungapereke ulemu wako kwa ena, Ndi zaka zako kwa ankhanza;