Proverbs 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, kodi udalonjeza kumlipirira mnzako chikole, kodi udaperekera mlendo chigwiriro?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, ngati waperekera mnzako chikole, ngati wapangana kulipirira mlendo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, ngati wamuperekera mnansi wako chikole, ngati walonjeza kumulipirira mlendo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, ngati waperekera mnzako cikole, Ngati wapangana kulipirira mlendo,