Proverbs 6:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
umphaŵi udzakugwira ngati munthu wachifwamba, usiŵa udzakufikira mwadzidzidzi ngati mbala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala, ndi kusauka kwako ngati munthu wachikopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
umphawi udzakugwira ngati mbala ndipo usiwa udzafika ngati munthu wachifwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala, Ndi kusauka kwako ngati munthu wacikopa.