Proverbs 6:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
maso onyada, pakamwa pabodza, manja opha munthu wosalakwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maso akunyada, lilime lonama, ndi manja akupha anthu osachimwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
maso onyada, pakamwa pabodza, manja akupha munthu wosalakwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso akunyada, lilime lonama, Ndi manja akupha anthu osacimwa;