Proverbs 6:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, uzitsata malamulo a atate ako, usasiye zimene adakuphunzitsa amai ako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, sunga malangizo a atate wako, usasiye malamulo a mai ako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, usunge malamulo a abambo ako; ndipo usataye zimene anakuphunzitsa amayi ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, sunga malangizo a atate wako, Usasiye malamulo a mako;