Proverbs 6:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja malamulowo ali ngati nyale, maphunzitsowo ali ngati kuŵala, madzudzulo a mwambo aja ndiwo mkhalidwe weniweni pa moyo wa munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti malangizo ndi nyali, malamulo ndi kuunika; ndi zidzudzulo za mwambo ndizo njira ya moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paja malamulo awa ali ngati nyale, malangizowa ali ngati kuwunika, ndipo chidzudzulo cha mwambo ndiwo moyo weniweni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti malangizo ndi nyali, malamulo ndi kuunika; Ndi zidzudzulo za mwambo ndizo njira ya moyo;