Proverbs 6:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidzakupulumutsa kwa mkazi woipa, zidzakuthandiza kuti usamvere mau osalala a mkazi wachiwerewere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zikutchinjiriza kwa mkazi woipa, ndi kulilime losyasyalika la mkazi wachiwerewere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kukupulumutsa kwa mkazi wadama, zimenezi zidzakutchinjiriza kwa mkazi wadama, ndi kukuthandiza kuti usamvere mawu oshashalika a mkazi wachiwerewere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zikucinjiriza kwa mkazi woipa, Ndi ku lilime losyasyalika la mkazi waciwerewere.