Proverbs 6:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndizo zimamchitikira wokaloŵerera mkazi wamwini. Aliyense wokhudza mkazi wotero adzalangidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho wolowa kwa mkazi wa mnzake; womkhudzayo sadzapulumuka chilango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndizo zimachitikira munthu amene amagonana ndi mkazi wa munthu wina. Aliyense wokhudza mkazi wotere adzalangidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco wolowa kwa mkazi wa mnzace; Womkhudzayo sadzapulumuka cilango.