Proverbs 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye iwe mwana wanga, popeza kuti wadziponya m'manja mwa mnzako, chita izi kuti udzipulumutse: nyamuka, pita msanga, ukampemphe kuti akumasule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chita ichi tsono; mwananga, nudzipulumutse; popeza walowa m'dzanja la mnzako, pita nudzichepetse, numdandaulire mnzako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono popeza iwe mwana wanga wadziponya mʼmanja mwa mnansi wako, chita izi kuti udzipulumutse: pita msanga ukamupemphe mnansi wako; kuti akumasule!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cita ici tsono; mwananga, nudzipulumutse; Popeza walowa m'dzanja la mnzako, Pita nudzicepetse, numdandaulire mnzako,