Proverbs 6:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja anthu sainyoza mbala, ikaba chifukwa cha njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu sanyoza mbala ikaba, kuti ikhutitse mtima wake pomva njala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paja anthu sayinyoza mbala ikaba chifukwa chakuti ili ndi njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu sanyoza mbala ikaba, Kuti ikhutitse mtima wace pomva njala;