Proverbs 6:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja nsanje imakalipitsa mwini mkaziyo, sachita chifundo akati alipsire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti nsanje ndiyo ukali wa mwamuna, ndipo sadzachitira chifundo tsiku lobwezera chilango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paja nsanje imachititsa mwini mkaziyo kukalipa, ndipo sadzachita chifundo pobwezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti nsanje ndiyo ukali wa mwamuna, Ndipo sadzacitira cifundo tsiku lobwezera cilango.