Proverbs 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzipulumutse monga imadzipulumutsira mphoyo kwa mlenje, monga imadzipulumutsira kwa wosaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzipulumutse wekha ngati mphoyo kudzanja la msaki, ndi mbalame kudzanja la msodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzipulumutse monga imachitira mphoyo mʼdzanja la mlenje, ndi monga imachitira mbalame mu msampha wa munthu wosaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzipulumutse wekha ngati mphoyo ku dzanja la msaki, Ndi mbalame ku dzanja la msodzi.