Proverbs 8:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Landirani malangizo anga m'malo mwa siliva, funitsitsani kudziŵa zinthu, osati kuthamangira golide wabwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Landirani mwambo wanga, si siliva ai; ndi nzeru kopambana ndi golide wosankhika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Landirani malangizo anga mʼmalo mwa siliva, nzeru zomvetsa zinthu mʼmalo mwa golide wabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Landirani mwambo wanga, si siliva ai; Ndi nzeru kopambana ndi golidi wosankhika.