Proverbs 8:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine nzeru ndimakhalira limodzi ndi kuchenjera. Ndimadziŵa zinthu ndipo ndimaganiza moyenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine Nzeru ndikhala m'kuchenjera, ngati m'nyumba yanga; ndimapeza kudziwa ndi zolingalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine nzeru, ndimakhala pamodzi ndi kuchenjera. Ine ndimadziwa zinthu ndiponso ndimalingalira zinthu bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine Nzeru ndikhala m'kucenjera, ngati m'nyumba yanga; Ndimapeza kudziwa ndi zolingalira.