Proverbs 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimathandiza mafumu polamulira ndine, olamulira ndimaŵathandiza ndine kulamula zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa ine mafumu alamulira; akazembe naweruza molungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndine amene ndimathandiza mafumu kulamulira. Ndimawathandiza olamulira kukhazikitsa malamulo olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa ine mafumu alamulira; Akazembe naweruza molungama.