Proverbs 8:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nzeru imakhala pa zitunda m'mbali mwa njira, imakaima pa mphambano za miseu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iima pamwamba pa mtunda, pa mphambano za makwalala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nzeru imayima pa zitunda mʼmbali mwa njira, imayima pa mphambano ya misewu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iima pamwamba pa mtunda, Pa mphambano za makwalala;