Proverbs 8:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimaŵapatsa chuma anthu ondikonda, ndi kudzaza nyumba zao zosungiramo chuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndionetse chuma akundikonda, chikhale cholowa chao, ndi kudzaza mosungira mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimapereka chuma kwa amene amandikonda ndi kudzaza nyumba zawo zosungiramo chuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndionetse cuma akundikonda, cikhale colowa cao, Ndi kudzaza mosungira mwao.