Proverbs 8:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndinalipo kale, pamene ankakhazikitsa zakumwamba, pamene ankalemba mzere wa malire a nyanja yozama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene anakhazika mlengalenga ndinali pompo; pamene analemba pazozama kwetekwete;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinalipo pamene Yehova ankakhazikitsa mlengalenga, pamene ankalemba malire a nyanja yozama,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene anakhazika mlengalenga ndinali pompo; Pamene analemba pazozama kwete kwete;