Proverbs 8:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene ankaika malire a nyanja kuti madzi ake asabzole malirewo, pamene ankaika maziko a dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Poikira nyanja malire ake, kuti madzi asapitirire pa lamulo lake; polemba maziko a dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene anayikira nyanja malire kuti madzi asadutse malirewo, ndiponso pamene ankayika malire a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poikira nyanja malire ace, Kuti madzi asapitirire pa lamulo lace; Polemba maziko a dziko,