Proverbs 8:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imafuula pafupi ndi zipata kumaso kwa mzinda, ndiponso pamakomo poloŵera, imati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pambali pa chipata polowera m'mudzi, polowa anthu pa makomo ifuula:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imafuwula pafupi ndi zipata zolowera mu mzinda, pa makomo olowera imafuwula kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pambali pa cipata polowera m'mudzi, Polowa anthu pa makomo ipfuula: