Proverbs 8:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵiyo nkuti ndili pambalipa ngati mmisiri wake, ndikumkondweretsa tsiku ndi tsiku, ndikusangalala pamaso pake nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinali pa mbali pake ngati mmisiri; ndinamsekeretsa tsiku ndi tsiku, ndi kukondwera pamaso pake nthawi zonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ine ndinali pambali pake ngati mmisiri; ndikumukondweretsa tsiku ndi tsiku, kusangalala nthawi zonse pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinali pa mbali pace ngati mmisiri; Ndinamsekeretsa tsiku ndi tsiku, Ndi kukondwera pamaso pace nthawi zonse;