Proverbs 8:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkasangalala m'dziko lake lokhalamo anthu, ndi kumakondwa nawo ana a anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kukondwera ndi dziko lake lokhalamo anthu, ndi kusekerera ndi ana a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkasangalala ndi dziko lake lonse ndiponso kumakondwera nawo anthu onse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kukondwera ndi dziko lace lokhalamo anthu, Ndi kusekerera ndi ana a anthu.