Proverbs 8:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwodala munthu amene amatchera khutu kwa ine, amene amakhala pakhomo panga tsiku ndi tsiku, amene amadikira pa chitseko changa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngwodala amene andimvera, nadikira pa zitseko zanga tsiku ndi tsiku, ndi kulinda pa mphuthu za makoma anga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodala munthu amene amandimvera, amene amakhala pa khomo panga tsiku ndi tsiku, kudikirira pa chitseko changa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngwodala amene andimvera, nadikira pa zitseko zanga tsiku ndi tsiku, Ndi kulinda pa mphuthu za makoma anga;