Proverbs 8:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu osadziŵa kanthunu, phunzirani nzeru, inu opusanu, khalani tcheru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Achibwana inu, chenjerani, opusa inu, khalani ndi mtima wozindikira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu amene simudziwa kanthunu khalani ochenjera; inu amene ndi opusa, khalani ndi mtima womvetsa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Acibwana inu, cenjerani, Opusa inu, khalani ndi mtima wozindikira;