Proverbs 8:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau anga ngoona kwa munthu womvetsa, ngokhoza kwa anthu odziŵa zinthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onsewo amveka ndi iye amene azindikira; alungama kwa akupeza nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa anthu ozindikira, mawu anga onse ndi woona; kwa anthu amene ali ndi nzeru zomvetsa zinthu, mawu angawo ndi okhoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onsewo amveka ndi iye amene azindikira; Alungama kwa akupeza nzeru.