Proverbs 9:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mwamunayo sadziŵa kuti kumeneko kuli imfa, kuti alendo ake aloŵa kale m'manda ozama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwamunayo sadziwa kuti akufa ali konko; omwe achezetsa utsiru ali m'manda akuya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma amunawo sadziwa kuti akufa ali kale komweko, ndi kuti alendo ake alowa kale mʼmanda akuya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwamunayo sadziwa kuti akufa ali konko; Omwe acezetsa utsiru ali m'manda akuya.