Proverbs 9:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Bwera, dzadyeko chakudya changa, ndipo udzamweko vinyo amene ndakonza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tiyeni, idyani chakudya changa; nimumwe vinyo wanga ndamsanganiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Bwerani, dzadyeni chakudya changa ndipo dzamweni vinyo amene ndakonza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tiyeni, idyani cakudya canga; Nimumwe vinyo wanga ndamsanganiza.