Proverbs 9:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wonyoza usamdzudzule, angadane nawe. Koma ukadzudzula munthu wanzeru, adzakukonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usadzudzule wonyoza kuti angakude; dzudzula wanzeru adzakukonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usadzudzule munthu wonyoza kuti angadzadane nawe; dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usadzudzule wonyoza kuti angakude; Dzudzula wanzeru adzakukonda.