Psalms 1:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa sali choncho, ali ngati mungu wouluzika ndi mphepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oipa satero ai; koma akunga mungu wouluka ndi mphepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sizitero ndi anthu oyipa! Iwo ali ngati mungu umene umawuluzidwa ndi mphepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oipa satero ai; Koma akunga mungu wouluka ndi mphepo.