Psalms 1:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake anthu ochimwa, Mulungu adzaŵazenga mlandu, adzaŵachotsa iwo pakati pa anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake oipa sadzaimirira pa mlanduwo, kapena ochimwa mu msonkhano wa olungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthu oyipa sadzatha kuyima pa chiweruzo, kapena anthu ochimwa mu msonkhano wa anthu olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace oipa sadzaimirira pa mlanduwo, Kapena ocimwa mu msonkhano wa olungama.