Psalms 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Chauta amaŵasamalira anthu ake, koma anthu ochimwa adzaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova adziwa mayendedwe a olungama; koma mayendedwe a oipa adzatayika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova amayangʼanira mayendedwe a anthu olungama, koma mayendedwe a anthu oyipa adzawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova adziwa mayendedwe a olungama; Koma mayendedwe a oipa adzatayika.